Anavar za jeni

PART 9
*****
...
Ngankhale Amati Mamuna Salila Ine Ndenkha Ndinalila Guys Azulu Si Anthu Tizingothokoza Kuti Kumalawi Kwathu Kuno Nkhondo Sitimayidziwa Koma Azathu Akujondiku Anava Kuning'ina..Anandithila Petro Uja Then Ndinayambamba Kupephela Pephelo Langa Lotsiliza Kuti Ambuye Awulandile Zimuwangawu. Ndili Nkati Mopephela Wina Anandiponda Kiki Yomwe Inasokoneza Pephelo Langa Kwa Mulengi Mwini Moyo Ndinakagwa Gada Then Anayamba Kufusana Kuti Machesi Ali Ndi Ndani Angondimalizililatu Basi Mwamwayi Ose Machesi Analibe Wina Anathamanga Kukatenga Chikuni Chomwe Chinkayaka Kuchokela Ku Nyumba Yanga Ija Anandiwotchela Ija Kuti Azindiwotcha Galimoto Ya Police Inatulukila Ose Ndikuthawa. Kundisiya Thupi Lose Lili Ndi Petro Ophatikiza Ndi Magazi Anga...Ndinagwada Pasi Kuthokoza Namalenga Kuti Anava Ndithu Pephelo Langa Ngakhale Ndinali Munthu Ochimwa Koma Mulungu Anakhala Ndithu Mbali Yanga.. Apolice Aja Ananditenga Ndikukandisiya Komwe Kunali Amalawi Anzanga Kuti Tidikile Ma Bus President Wathu Athumiza Ma Bus Adzatinyamule Tibwelele Kumudzi Ndinasangalala Kwambili Ndinali Ndi Chisangalaso Chophatikizana Ndi Chisoni Coz Katundu Wanga Yese Yemwe Ndagwilila Tchito For 2 Years Anawonongeka Ndi Moto Mbali Inayi Ndimasangalala Kuti Ndapulumuka Ku Ifa Bwezi Ndikuyimba Ndi Angelo.. Ndakayikaso Ngati Mulengi Akanandilandila Bwino Paja Ndinathawa Mimba Yanga Kumudziku...
.
(Madalo)
Moyo Unapitilila Kukhala Ovuta Zinthu Zimandiyendela Pang'ono Kwambili. Ka Bussines Ka Zova Kaja Ndinadukaso Chifukwa Choti Ndimasowa Ndlama Yolipila Rent Ndinangotenga Ndlama Ya Bussiness Yose Ndikulipila Lent Kuti Atleast Tizipezako Pogona Pokha. Zinthu Zinafika Pondivuta Zedi Ben Jny Atadwala Mwosadziwika Bwino Ndinathamangila Naye Ku Chipatala Cha Boma Atamuyesa Anamupeza Ndi Malungo Akulu Koma Anandiwuza Kuti Mankhwala Kuchipatalaku Kulibe Ndipite Naye Ku Chipatala Cha Private. Ndinamutengela Ben Mwana Wanga Ku Chipatala Cha Private Komwe Analindila Chithandizo Bwinolomwe Koma Anamupanga Adimiti Bill Itabwela Ndinalakalaka Kulowa Pasi Anandipatsa Bill Ya K50,000 Pomwe Ine Ndinali Ndi K1,500 Yokga Basi Muntu Unandikulila Where Wil I Get The Remening Money? Misozi Inatsika Maso Mwanga Ndinalakalaka Bambo Anga Akanakhala moyo Kapena Sir Ben Akanakhalapo Kuti Alipo Bwezi Mavuto Otele Sindinakumane Nawo Mutu Unandikulila Ndilowela Kuti??....
<<<<..........................
.pepani kafupi part ina mawa mamawa.
...........

Anavar za jeni

anavar za jeni

Media:

anavar za jeni

http://buy-steroids.org